Quantcast
Channel: Health | Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 2462

Chimbudzi cha K15.9 million ku Rumphi chagwa

$
0
0

Chimbudzi cha ndalama zokwana K15.9 million chomwe khonsolo ya Rumphi inamanga pa nyumba yodikilira amayi apakati pa chipatala cha Rumphi chagwa masanawa. Wapampando wa komiti ya zaumoyo pachipatalachi a Manase Mhango wati akukaikira kuti chimbudzichi chagwa kamba koti sichinamangidwe molimba.   A Mhango ati pakadali pano adziwisa kale DC wabomali za nkhaniyi ndipo ati palibe […]

The post Chimbudzi cha K15.9 million ku Rumphi chagwa appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 2462

Trending Articles



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>