Wapolisi wina ku Rumphi wadziponya mu mtsinje wa South Rukulu omwe pano wadzadza ndikusefukira mbali zina m’bomali. Mneneri wa polisi mchigawo chakumpoto a Maurice Chapola, angotsimikiza zoti alandira lipoti lakusowa kwa a Ngamanya Mbale koma anakana kuyankhulapo zambiri ponena kuti kafukufuku wawo ali mkati. Koma yemwe watitsina khutu wati a Mbale adziponya mu mtsinjewu […]
The post Wapolisi azipha poziponya munsinje kamba ka chibwezi appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.↧