Quantcast
Channel: Health | Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 2462

Madam Chakwera ali ku Switzerland ku msonkhano wokambirana zothesa matenda a TB

$
0
0

Mayi wa fuko lino,Monica Chakwera yemwenso ndi kazembe pankhani yolimbana ndi matenda a chifuwa cha TB kuno ku Malawi akuyembekezeka kuyakhula nthumwi pa nkhani za umoyo zomwe zikusokhana  mdziko la Switzerland komwe ali nawo pa msonkhano  waukulu pa dziko lonse okambirana njira zolimbana ndi matenda a chifuwa cha  chachikulu cha TB (World Health Summit). Madam […]

The post Madam Chakwera ali ku Switzerland ku msonkhano wokambirana zothesa matenda a TB appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 2462

Trending Articles



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>